CHATSOPANO! Dinani kuti Mumasulire

Tsopano Zomasulira za Google zikugwira ntchito pa pulogalamu iliyonse.

Translate app
×
×

Lankhulani ndi dziko lonse

Kugwirizana ndi anthu a m'malo ndi chikhalidwe chosiyana ndi chanu.

Onerani vidiyo
Pezani zimenezi pa Google Play Zikupezeka mu Sitolo ya Mapulogalamu
mapu a dziko lonse

Tidzakhala nanu nthawi zonse

  • FONI YAM'MANJA
  • PALIBE INTANETI
  • KUMPYUTA

Kukhala ndi Pulogalamu Yomasulirira kuli ngati kukhala ndi munthu wokuthandizani kumasulira chinenero m'nthumba mwanu.

Palibe intaneti? Musadandaule. Ndizothekabe ngakhale foni yanu itakhala kuti sinalumikizidwe ku intaneti, chongafunika n'kuitchera kuti sili pa intaneti.

Zomasulira zingathandize kwambiri pa mawu ataliatali, ovuta kuwatchula, ngakhalenso pa madokyumenti amene achita kulowetsedwa mukompyuta kapena foni.

Yankhulani, tolani zithunzi, lembani kapena tayipani.
Kusankha n'kwanu

Lankhulani ndi munthu amene amalankhula chinenero china.
Zizindikiro, ndandanda, ndi zina zotero. Ingolozetsani kamera yanu pamawuwo ndipo amasuliridwa nthawi yomweyo. Simukufunikira kukhala ndi intaneti.
Zilembo zimene zingalembedwe mosavuta pamanja sizikugwirizana ndi kiyibodi yanu.
Tangolembani mawu amene mukufuna kumasulirawo.
  • YANKHULANI
  • JAMBULANI CHITHUNZI
  • LEMBANI
  • TAYIPANI
Pezani zimenezi pa Google Play Zikupezeka mu Sitolo ya Mapulogalamu